From the recording Imvani Pemphero Langa

In cart Not available Out of stock

A line from the famous Lord's prayer says
'Your will be done on earth as it is in heaven'. This song talks reminds us that inspite of challenges we face daily in our faith walk, our cry should be 'Lord let you will be done'. His ways are not our ways and His thoughts are not our thoughts so we may never come to fully understand His purpose and intentions when He allows us to experience different situations in our lives. Isaiah 55:8 and Matthew 6:10

Lyrics

Nthawi zambiri tikamakhala mdzikoli
Nkumaona zochitika sitimvetsa
Masautso osasimbika kwa anthu
Koma ife tikumbukira
Ndikupempha kuti

Kufuna kwanu kuchitidwe
Monga kumwamba
Mutiphunzitse tikumbukire
Kuti simumasintha
Pamtendere,(pena) pa mavuto mumakhala ndi cholinga
Choncho Mbuye kufuna kwanu kuchitidwe

Njira zanu sinjira zathu palibe angamvetse
Angakhale tilakalaka kuti tidziwe
Maganizo anu siathu ichi tichidziwa
Koma ife posamvetsetsa
Tilore kuti Mbuye