From the recording Imvani Pemphero Langa

In cart Not available Out of stock

Christ said that He has gone to heaven to prepare for us a place. He will return one day to take us there (John 14:1-3).
We look forward to meeting those loved ones who have gone on before us. A city with streets of gold awaits those who have believed in Him and got saved!

Lyrics

Kumwamba nkwabwino
Nkumene Ambuye apita
Kukatikonzera malowo
Ndi mzinda wabwino

Ambuyewo anakwera
Kunka mmwamba kukakonzatu
Malo omwe tikafika
Tizakhala anthu okondwa

Mzinda wake wokongola
Wa golidi komanso siliva
Nkomwenso tikaonana
Ndi oyera/abale anafa kalero

Mzinda wake wokongola
Wa golidi komanso siliva
Nkomwenso tikakomana /tikaonana
Ndi amayi/abambo anafa kalero