0:00/???
  1. Kunali Nkhani

From the recording Imvani Pemphero Langa

In cart Not available Out of stock

There is always joy in heaven when a sinner repents and comes back home into the kingdom of God. The story of the prodigal son reminds us of this wonderful news.

Lyrics

Kunali nkhani tsiku lina
Ku dziko lija la kumwamba
Kodi mwamva mwana uja/bambo/mayi
Lero lino wapulumuka
Atalandira mpulumutsi
Tikondwere tisangalale

Tsegulani bukhu lija
Dzina lake lembanimo
Anatayika/anasochera lero wapeza
Kuno kumwamba tasangalala

Nanga iwe uli apo
Uti bwanji ndi nkhani iyi
Mbuye Yesu ali pa khomo
La mtima wako akugogoda
Uchedweranji kumtsegulira
Kuti kumwamba asangalale