From the recording Imvani Pemphero Langa
A time to praise and exalt the King of kings. Seek His face and declare His majesty.
Lyrics
Mbuye tifuna nkhope yanutu
Kuti yiti wunikire
Ndikutionetsera njira
Kuti tikhale wozindikira
Tikukwezani tikutamani
Palibe wina wonga inu
Muyenera kulandira
Matamando
Yesu mwazi munakhetsa
Utitsuke nutikonze
Ndipo ife tidzayeretsedwa
Ndikukhala wotetezedwa