0:00/???
  1. Mawu A Mulungu

From the recording Imvani Pemphero Langa

In cart Not available Out of stock

Mawu A Mulungu literally means the word of God. The song encourages us to take responsibility for what the word of God instructs us to do. In otherwords we should be doers of the word and not only hearers.

Lyrics

Mawu a Mulungu
vs 1
Mawu a Mulungu alalikidwa
Wakumva wamva ulaliki
Tiwasanthule m’mitima mwathu
Tikaterotu tidalitsika

Chorus
Ziri kwa ife kuchita nawo
Mmene afunira ambuye wathu
Iye atikonda anatiferanso
Imfa yoopsa yapamtanda

vs 2
Lapatu m’bale nthawi ndiyomweyi
Poti ukafa mwawi palibe
Yesu atitu idza kwa ine
Inetu ndine njira ya moyo

vs 3
Mau a Mulungu nchakudya chake
Cha moyo wathu wauzimu
Tikawerenga alankhula nafe(Mlungu)
Tikawachita atidalitsa