From the album Imvani Pemphero Langa

In cart Not available Out of stock

God is our strength upon whom we depend

Lyrics

Mbuye Ndinu Mphamvu yathu

vs 1
Mbuye ndinu mphamvu yathu
Tidalira kwa inu
Chigonjetso tichipeza
Sikwinanso koma kwa inu

Chorus
Nthawi zonse tifuna inu
Kuti Mbuye mutsogolere
Popeza inu mumateteza
Komanso inu simulephera

vs 2
Mau anu ndiwo chida
Choopsatu kwambiritu
Amaphwasula malinga onse
A woipa wotineneza