From the recording Imvani Pemphero Langa
Do not fret because of evil men or
Be envious of those who do wrong
For like grass they will soon wither
Like green plant they will soon die away
(Psalm 37:1-2,4, 6)
Lyrics
Mtima Wanga Usavutike
vs 1
Mtima wanga usavutike
Chifukwa cha wochita zoipa
Pakuti adzawamweta msanga ,Yehova
Adzawamweta mongatu msipu
Chorus
Udzikondweretsenso mwa Yehova
Ndipo Iye adzakupatsa zokhumba
Mtima wako
vs
Pakutitu wochitatu zoipa
Onse ndithu adzadulidwa
Koma woyembekezera Yehova, iwowa
Adzalandira dziko la pansi