From the recording Imvani Pemphero Langa

In cart Not available Out of stock

God is not pleased with death of a sinner.
Today when you hear his word do not harden your heart.
Let Christ take control of your life

Lyrics

Tamvani Inu Abale
vs 1
Tamvani inu abale
Mlungu ali kunena kuti
Sakondwera ndi imfa
Ya munthutu wochimwa

Chorus
Mukamva mawu ake lero
Musalimbitse mtima
Lolani kuti Yesu
Alamulire moyo wanu

vs 2
Kumbukirani kuti
Mphoto ya uchimo ndi imfa
Koma mphatso ya ulere
Ya Mulungu ndiyo moyo wosatha