From the recording Imvani Pemphero Langa
Christmas song.
Let us rejoice for unto us a child is born
A son has been given
Lyrics
Tikukondwera
Chorus
Tikukondwera
Watibadwira
Mwana wa Mlungu
M’nkhola la ng’ombe
vs 1
Timuyimbire ndikumtamanda
Timugwadire ndi kumpembeza
Yesu Ambuye ndi mpulumutsi/chipulumutso
vs 2
Timulambire,ndi kumukwezeka
Timuthokoze,ndikumnyadira
Kristu Ambuye,watifikira